N’ciani Catsopano?

2024-05-09

NYIMBO ZOPEKEDWA KOYAMBA

“Uthenga Wabwino”! (Nyimbo ya pa Msonkhano Wacigawo wa 2024)

Kuyambila m’zaka za zana loyamba mpaka masiku ano, mwacimwemwe anthu akhala akulalikila uthenga wabwino. Uthengawo ni wofunika kwambili kuposa uthenga wina ulionse cifukwa umakamba za nchito imene Yesu iye mwini anaiyambitsa, komanso mmene angelo amamuthandizila pa nchitoyi.

2024-05-01

NSANJA YA MLONDA

Kodi Tingawapeze Kuti Malangizo Odalilika

Onani mmene mungapangile zisankho zabwino zimene zidzakuthandizani limodzi na banja lanu kukhala na tsogolo labwino.

2024-04-19

KHALANI MASO!

Kodi Nkhondo Zidzatha Liti?—Kodi Baibo Ikutipo Ciyani?

Posacedwa, nkhondo zonse zidzatha. Baibo imafotokoza mmene nkhondo zidzathela.

2024-04-16

NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA

Zimene Zingakuthandizeni Mukasamukila mu Mpingo Watsopano

Akhristu ambili akwanitsa kuzoloŵela mpingo watsopano. N’ciyani cimathandiza munthu kuzoloŵela mpingo watsopano? Onani mfundo zinayi zimene zingakuthandizeni.

2024-04-16

NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA

Mafunso Ocokela kwa Oŵelenga​—July 2024

Kodi “mkazi” wochulidwa pa Yesaya 60:1 ndani, nanga ‘adzaimilila’ motani, ndipo ‘adzaonetsa kuwala kwake’ motani?

2024-04-16

NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA

Khalanibe Maso mwa Kuŵelenga Baibo Mwakhama

2024-04-16

NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA

July 2024

Magazini ino ili na nkhani zophunzila mu mlungu wa September 9–​October 6, 2024.