Pitani ku nkhani yake

Nowa Anali Womvera Chifukwa cha Chikhulupiriro

Dziwani mmene kumvera Yehova komanso chikhulupiriro zinathandizira Nowa kuti apulumuke Chigumula. Nkhani yochokera pa Genesis 6:1–8:22; 9:8-16.

Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi

TSANZIRANI CHIKHULUPIRIRO CHAWO

Nowa—“Anayenda Ndi Mulungu Woona”

Kodi Nowa ndi mkazi wake anakumana ndi mavuto otani polera ana awo? Kodi anasonyeza bwanji kuti anali ndi chikhulupiriro pomanga chingalawa?

NSANJA YA OLONDA

Anapulumutsidwa “Pamodzi ndi Anthu Ena 7”

Kodi Nowa ndi banja lake anapulumuka bwanji chigumula chomwe chinachitika padziko lonse lapansi?

KUYANKHA MAFUNSO A M’BAIBULO

Kodi Nkhani ya Nowa Komanso Chigumula Ndi Nthano Chabe?

Baibulo limafotokoza kuti Mulungu anabweretsa chigumula kuti awononge anthu oipa. Kodi Baibulo lili ndi umboni wotani wotsimikizira kuti linalembedwadi ndi Mulungu?

NSANJA YA OLONDA

Inoki: ‘Mulungu Anakondwera Naye’

Ngati mumasamalira banja kapena zimakuvutani kuti muzichita zinthu molimba mtima, mukhoza kuphunzira zambiri pa chitsanzo cha Inoki.

KUYANKHA MAFUNSO A M’BAIBULO

Kodi Anefili Anali Ndani?

Baibulo limafotokoza kuti anali “ziphona zakalelo, amuna otchuka.” Kodi timadziwa zotani zokhudza Anefili?

ZIMENE TINGAPHUNZIRE MUNKHANI ZA M’BAIBULO

Chingalawa cha Nowa

Angelo oipa atakwatira akazi padzikoli anabereka ana amene ankavutitsa anthu. Chiwawa chinali ponseponse. Koma Nowa sankachita nawo zoipa. Iye ankakonda Mulungu komanso ankamumvera.