Pitani ku nkhani yake

Yakobo Anali Munthu Wokonda Mtendere

Onani zimene Yakobo anachita kuti akhale pamtendere ndi anthu ena. Nkhaniyi ikuchokera pa Genesis 26:12-24; 27:41–28:5; 29:16-29; 31:36-55; 32:13-20; 33:1-11.

Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi

ZIMENE TINGAPHUNZIRE MUNKHANI ZA M’BAIBULO

Yakobo Analandira Madalitso

Isaki ndi Rebeka anali ndi ana awiri amapasa ndipo mayina awo anali Esau ndi Yakobo. Esau anali wamkulu ndipo ankayenera kulandira madalitso. N’chifukwa chiyani anasinthanitsa madalitsowo ndi mbale ya mphodza?

ZIMENE TINGAPHUNZIRE MUNKHANI ZA M’BAIBULO

Yakobo ndi Esau Anagwirizananso

Kodi Yakobo anatani kuti mngelo amudalitse? Nanga anatani kuti akhululukirane ndi Esau?