Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale—Kuphunzira Baibulo Mokambirana

Bukuli lakonzedwa kuti lizigwiritsidwa ntchito pophunzira Baibulo ngati njira imodzi imene timagwiritsa ntchito pophunzira Baibulo ndi anthu kwaulere.

Pepani, palibe mawu ofanana ndi omwe mwasankha

Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi

MAFUNSO OFUNSIDWA KAWIRIKAWIRI

Kodi Phunziro la Baibulo lomwe a Mboni za Yehova Amachititsa Limakhala Lotani?

Mukamaphunzira Baibulo kwaulere ndi a Mboni za Yehova, mungagwiritse ntchito Baibulo lililonse limene mukufuna. Mungapemphenso onse a m’banja lanu kapena mnzanu wina aliyense kuti akhale nanu pa phunzirolo.