GALAMUKANI! January 2013 | Mmene Mungalerere Ana Anu Kuti Asakhale Odzikonda

Mmene tingapewere zinthu zitatu zimene makolo ena amalakwitsa polera ana.

Zochitika Padzikoli

Werengani kuti mudziwe nkhani zomwe zikuchitika m’madera osiyanasiyana padziko lapansi.

MFUNDO ZOTHANDIZA MABANJA

Zimene Mungachite Kuti Muzimasukirana ndi Mwana Wanu

Kodi mumakhumudwa kwambiri chifukwa cholephera kulankhulana bwino ndi mwana wanu? Kodi n’chiyani chimene chimachititsa kuti muzivutika kulankhulana naye?

KUCHEZA NDI ANTHU

Wasayansi Akufotokoza za Chikhulupiriro Chake

Werengani kuti mumve mfundo za sayansi zimene anagwiritsa ntchito komanso chifukwa chake amakhulupirira Mawu a Mulungu.

NKHANI YAPACHIKUTO

Mmene Mungalerere Ana Anu Kuti Asakhale Odzikonda

Werengani nkhaniyi kuti mudziwe njira zitatu zimene zingathandize kuti ana anu asakhale odzikonda.

ANTHU NDI MAYIKO

Dziko la Cameroon

Werengani nkhaniyi kuti mudziwe mbiri komanso chikhalidwe cha anthu a ku Cameroon.

ZIMENE BAIBULO LIMANENA

Paradaiso

Kodi Paradaiso adzakhala kumwamba kapena padziko lapansi pompano? Kodi ndani amene andzakhale m’Paradaiso?

KODI ZINANGOCHITIKA ZOKHA?

Mbalame Yotha Kuuluka Ulendo Wautali

Werengani nkhaniyi kuti mudziwe za mbalame inayake yogometsa kwambiri imene imayenda ulendo wautali masiku 8 okha.

Zina zimene zili pawebusaiti

Kodi Ndizitani Ngati Ena Akundichitira Zachipongwe?

Werengani nkhaniyi kuti mudziwe tanthauzo la kuchitiridwa zachipongwe komanso zimene mungachite ngati mutachitiridwa zachipongwezo.

Solomo Anachita Zinthu Mwanzeru

Pezani zimene zikusowa pachithunzichi, lumikizani timadonthoti ndipo chikongoletseni ndi chekeni.