NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA) April 2024

M’magaziniyi muli nkhani zophunzira kuyambira June 10–​July 7, 2024.

NKHANI YOPHUNZIRA 14

‘Tiyesetse Mwakhama Kuti Tikhale Aakulu Mwauzimu’

Nkhaniyi tidzaiphunzira mlungu wa June 10-16, 2024.

NKHANI YOPHUNZIRA 15

Muzikhulupirira Kwambiri Gulu la Yehova

Nkhaniyi tidzaiphunzira mlungu wa June 17-23, 2024.

NKHANI YOPHUNZIRA 16

Zimene Tingachite Kuti Tizisangalala Kwambiri Tikamalalikira

Nkhaniyi tidzaiphunzira mlungu wa June 24-30, 2024.

NKHANI YOPHUNZIRA 17

Musachoke M’Paradaiso Wauzimu

Nkhaniyi tidzaiphunzira mlungu wa July 1-7, 2024.

MBIRI YA MOYO WANGA

Kufooka Kwanga Kwachititsa Kuti Mphamvu za Mulungu Zionekere

M’bale Erkki Mäkelä akufotokoza mmene Yehova wamuthandizira pa mavuto osiyanasiyana omwe wakhala akukumana nawo pa utumiki wake, monga pamene anali mmishonale kudera lomwe kunkachitika nkhondo ku Columbia.

Kodi Mukudziwa?

N’chifukwa chiyani anthu a mitundu ina anali m’gulu la asilikali a Mfumu Davide?