NSANJA YA OLONDA Na. 1 2019 | Kodi Mulungu Ndi Ndani?

Werengani nkhaniyi kuti mumve mayankho a mafunso 6 omwe angakuthandizeni kukhala pa ubwenzi ndi Mulungu.

Kodi Mulungu Ndi Ndani?

Kudziwa Mulungu ndi poyambira pabwino ngati tikufuna kukhala naye pa ubwenzi. Koma kodi mungamudziwe bwanji?

Kodi Dzina la Mulungu Ndi Ndani?

Kodi mumadziwa kuti Mulungu ali ndi dzina limene limamusiyanitsa ndi milungu ina?

Kodi Mulungu Ali Ndi Makhalidwe Otani?

Kodi makhalidwe aakulu a Mulungu ndi ati?

Kodi Mulungu Wachita Zinthu Ziti?

Mungadabwe kumva zimene Mulungu wachita kuti anthu adzakhale ndi tsogolo labwino.

Kodi Mulungu Adzachita Chiyani?

Werengani nkhaniyi kuti mumve mmene zinthu zidzakhalire Ufumu wa Mulungu ukadzayamba kulamulira.

Kodi Kudziwa Mulungu Kungakuthandizeni Bwanji?

Kodi anthu amene amayesetsa kukhala pa ubwenzi ndi Mulungu adzapeza madalitso otani?

Mungathe Kukhala pa Ubwenzi ndi Mulungu

Werengani nkhaniyi kuti mudziwe zinthu 4 zimene zingakuthandizeni kukhala pa ubwenzi ndi Mulungu.