NSANJA YA OLONDA Na. 6 2016 | Masomphenya Otithandiza Kumvetsa za Kumwamba
Baibulo lingakuthandizeni kudziwa za zinthu zosaoneka.
NKHANI YAPACHIKUTO
Mafunso Okhudza Mmene Zilili Kumwamba
Tikhoza kupeza mayankho odalirika a mafunso okhudza kumwamba.
NKHANI YAPACHIKUTO
Masomphenya Osonyeza Amene Ali Kumwamba
Kodi Malemba amanena zotani zokhudza Yehova Mulungu, Yesu Khristu ndiponso angelo okhulupirika?
Zimene Tingaphunzire kwa Mbalame
Mbalame zimasonyeza kuti Mulungu ndi mlengi wanzeru komanso zimatithandiza kuganizira zinthu zofunika kwambiri.
Lefèvre d’Étaples Ankafuna Kuti Anthu Wamba Adziwe Mawu a Mulungu
Kodi anakwanitsa bwanji kumasulira Baibulo m’Chifulenchi ngakhale kuti ankatsutsidwa?
MBIRI YA MOYO WANGA
Ndilibe Manja Koma Ndinatha Kulandira Choonadi cha M’Baibulo
Mnyamata wina amene anachita ngozi yoopsa anapeza umboni womuthandiza kukhulupirira kuti kuli Mulungu.
Kodi Baibulo Limanena Zotani?
Kodi Mulungu amamvetsera ndiponso kuyankha mapemphero anu?
Zina zimene zili pawebusaiti
Kodi Mulungu Analenga Mdyerekezi Kuti Azitiyesa?
Kodi Satana anachokera kuti? Werengani nkhaniyi kuti mudziwe chifukwa chake Yesu ananena kuti Mdyerekezi “sanakhazikike m’choonadi.”