NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA) June 2022

M’magaziniyi muli nkhani zophunzira kuyambira August 8–September 4, 2022.

NKHANI YOPHUNZIRA 27

“Yembekezera Yehova”

Kodi Mukudziwa?

Kodi Aroma ankalola kuti munthu amene waphedwa popachikidwa pamtengo, ngati mmene zinalili ndi Yesu, aikidwe m’manda ngati anthu ena onse?

Kodi Mukudziwa?

Kodi kale anthu ankadziwa bwanji pamene payambira mwezi kapena chaka?