NSANJA YA OLONDA September 2009 Kodi Mulungu Amafuna Kuti Mukhale Wolemera? Chuma Chimene Mulungu Amapereka Kodi Munthu Akakhala Wosauka Ndiye Kuti Sakukondedwa ndi Mulungu? Kodi Ndalama Zimathandiza Munthu Kukhala Wosangalaladi? Mayi Wosauka Koma Wosangalala Kodi Adamu ndi Hava Anali Anthu Enieni? Werengani za Baibulo Lamakedzana Kodi Mukudziwa? Woweruza Wachilungamo Kodi Muyenera Kuchita Chiyani Mukakhumudwitsidwa? Zodabwitsa Zimene Zinachitika pa Pentekosite Chuma cha M’nyanja Yaikulu ya ku Central America ZIMENE OWERENGA AMAFUNSA Kodi Yesu Ankatanthauza Chiyani Pamene Ananena Kuti Iye ndi Atate Ake Ndi Amodzi? Zimene Zingathandize Amishonale Kuti Zinthu Ziwayendere Bwino