Pitani ku nkhani yake

Kuona Malo ku Beteli

Tikukuitanani kuti mudzaone maofesi athu a nthambi omwenso amadziwika kuti Beteli. Ku maofesi athu ena kulinso malo achionetsero omwe mukhoza kuona nokha popanda wokutsogolerani.

Kuyambiranso Kuona Malo: M'mayiko ambiri, anthu adzayambiranso kuona malo m'maofesi athu a nthambi kuyambira pa 1 June, 2023. Kuti mudziwe zambiri, lankhulani ndi abale a ku nthambi yomwe mukufuna kukaonayo. Komabe, musapite kukaona malo ngati mwapezeka ndi COVID-19 kapena ngati muli ndi zizindikiro za chimfine kapenanso ngati posachedwapa munakumana ndi munthu amene wapezeka ndi COVID-19.

Angola

Rua de Talatona N°1 (Próximo da Angola Telecom)

LUANDA SUL

ANGOLA

+244 222-460-192

+244 222-460-211

Onani Mapu

Kuona Malo

Lolemba mpaka Lachisanu

8:00 a.m. mpaka 11:00 a.m. ndi 1:00 p.m. mpaka 4:00 p.m.

Nthawi yonse: Mphindi 45

Zimene Timachita

Timamasulira mabuku a nkhani za m’Baibulo m’Chichokwe, Chikongo, Chimbundu, Chingangela, Chinyaneka ndi Chiumbundu. Timatumiza magazini pafupifupi 1 miliyoni chaka chilichonse m’mipingo yoposa 1,000.

Koperani pepala losonyeza ofesi yathu.