Mboni za Yehova Padziko Lonse

Guadeloupe

Mfundo Zachidule—Guadeloupe

  • 396,000—Chiwerengero cha anthu
  • 8,488—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 118—Mipingo
  • Pa anthu 47 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

NKHANI

A Mboni Akugwira Mwakhama Ntchito Yothandiza Anthu Omwe Anakhudzidwa Ndi Mphepo Zamkuntho

Maofesi a Nthambi a Mboni za Yehova akufotokoza zimene akuchita pothandiza komanso kutonthoza mwauzimu anthu okhudzidwa ndi mphepo yamkuntho ya Irma ndi Maria.