Mboni za Yehova Padziko Lonse

Hungary

  • Mtsinje wa Danube, Budapest, Hungary—Akugawira mabuku othandiza kuphunzira Baibulo

Mfundo Zachidule—Hungary

  • 9,597,000—Chiwerengero cha anthu
  • 21,332—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 283—Mipingo
  • Pa anthu 453 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

NKHANI

Pamalo Osungirako Mbiri Yokhudza Nkhanza za Chipani cha Nazi ku Hungary Panaonetsedwa Chithunzi Cholemekeza a Mboni Amene Anaphedwa

Pofuna kukumbukira a Mboni za Yehova 4 amene anaphedwa chifukwa chokana kuchita zinthu zosagwirizana ndi chikumbumtima chawo panthawi ya nkhondo yachiwiri ya padziko lonse, Pamalo Osungira Mbiri Yokhudza Nkhanza za Chipani cha Nazi panaonetsedwa chithunzi cha Amboniwo.