Mboni za Yehova Padziko Lonse

Niger

  • Dera la Haro Banda, Niamey, Niger​—Akupatsa munthu kabuku kofotokoza nkhani za m’Baibulo

Mfundo Zachidule—Niger

  • 27,066,000—Chiwerengero cha anthu
  • 373—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 9—Mipingo
  • Pa anthu 83,796 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

Anadzipereka ndi Mtima Wonse Kumadzulo kwa Africa

Kodi n’chiyani chinalimbikitsa Akhristu ena ku Ulaya kuti asamukire kumadzulo kwa Africa, nanga zinthu zikuwayendera bwanji kumeneko?