Pitani ku nkhani yake

BAIBULO LIMASINTHA ANTHU

Juan Pablo Zermeño: Yehova Anandithandiza Kukhala ndi Moyo Watanthauzo

Juan Pablo Zermeño: Yehova Anandithandiza Kukhala ndi Moyo Watanthauzo

Anthu ambiri amakhala ndi moyo wamtendere komanso watanthauzo akadzipereka kwa Yehova ngakhale kuti anakumana ndi mavuto akuluakulu ali ana. Juan Pablo anasankha kusiya masewera a nkhonya ndipo panopa akukhala moyo watanthauzo.