Pulogilamu ya Msonkhano Wacigawo wa 2021

Tsiku Loyamba

Pulogilamu ya tsiku loyamba yazikidwa pa Luka 17:5—“Tiwonjezeleni cikhulupililo.”

Tsiku Laciŵili

Pulogilamu ya tsiku laciŵili yazikidwa pa Yuda 3—‘Menyani mwamphamvu nkhondo ya cikhulupililo.’

Tsiku Lacitatu

Pulogilamu ya tsiku lacitatu yazikidwa pa Mateyu 21:21—‘Ngati muli ndi cikhulupililo . . . Zidzacitikadi.’

Mawu kwa Osonkhana

Mawu othandiza kwa opezeka pa msonkhano wacigawo.