GALAMUKA! Na. 1 2019 | Kodi Zidzatheka Kukhala Mwamtendele ndi Motetezeka pa Dzikoli?

Onani zina mwa zinthu zimene zimatilepheletsa kukhala mwamtendele ndi motetezeka. Onaninso cimene cidzafunika kuti dzikoli likhale malo okhalapo amtendele komanso otetezeka.

Zimene Zapangitsa Anthu Kusakhala Mwamtendele ndi Motetezeka

Kuposa kale lonse, masiku ano pali mavuto ambili amene apangitsa kuti tisakhale motetezeka. Kodi pali njila yowathetsela?

Kugwebana na Gwelo Leni-Leni la Mavuto a Anthu

Kaamba ka kupanda ungwilo kwathu, timakumana na mavuto ambili. Kodi tingapeze kuti thandizo?

Kuphunzitsa Anthu Makhalidwe Abwino

Makhalidwe abwino ni ofunikila kuti tikhale pa mtendele komanso motetezeka

Mbili ya Ricardo na Andres

Poyamba, Ricardo na Andres anali kusoŵetsa mtendele maneba awo. Koma manje amalimbikitsa mtendele. Onani mmene Baibo inasinthila umoyo wawo.

‘Ndipo Mtendelewo Sudzatha’

Kodi Ufumu wa Mulungu N’ciani?

Mu Ufumu wa Mulungu, pa Dziko “Padzakhala Mtendele Woculuka”

Ufumu wa Mulungu udzabweletsa mtendele na mgwilizano pa dziko lonse lapansi.

Kodi Munadzifunsapo?

Kodi mungapeze kuti mayankho pa mafunso anu a m’Baibo?