Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

NSANJA YA MLONDA Na. 3 2020 | Madalitso Osatha Ocokela kwa Mulungu Wacikondi.

Kodi ni madalitso otani amene Mulungu analonjeza anthu? Kodi mungawadalile Mawu ake? Nkhani zotsatila zidzafotokoza ena mwa malonjezo a Mulungu. Zidzafotokozanso cifukwa cake mungakhulupilile malonjezowo, komanso zimene mungacite kuti mulandile madalitso olonjezedwa, na kukhala wacimwemwe.

 

Mungasangalale na Madalitso Osatha Ocokela kwa Mulungu Wacikondi

Kodi mumalakalaka kukhala m’dziko limene mulibe nkhondo, upandu na matenda? Limeneli si loto cabe koma ni lonjezo locokela kwa Mulungu.

Mlengi Wathu Wacikondi Amasamala za Ife

Monga tate wacikondi, Mulungu amasamalila banja lake. Motani?

Mmene Mlengi Wacikondi Amatiuzila za Malonjezo Ake

Kodi Mulungu anawaseŵenzetsa bwanji aneneli kulemba uthenga wake kwa ife?

Kodi Mawu a Mulungu Anasinthidwa?

Onani zimene akatswili apeza ponena za Baibo imene tili nalo masiku ano.

Timadziŵa za Mulungu Kucokela kwa Aneneli Ake

Aneneli atatu okhulupilika atithandiza kudziŵa za Mulungu na zimene tingacite kuti tilandile madalitso ake.

Pitilizani Kupemphela Kuti Mulungu Akuyanjeni

Kodi tingapemphele bwanji kuti Mulungu atimvele na kutidalitsa?

Madalitso kwa Anthu Omvela Mulungu

Onani mfundo ziŵili izi za mmene tingapezele madalitso cifukwa comvela Mulungu.

Mmene Tingaonetsele Cikondi kwa Anthu Anzathu

Si nthawi zonse pamene zimakhala zopepuka kuonetsa cikondi kwa ena, koma n’zotheka.

Madalitso kwa Amene Amathandiza Ofunikila Thandizo

Kodi kuthandiza munthu wofunikila thandizo kungatipangitse bwanji kukhala oyanjidwa na Mulungu, komanso kulandila madalitso ake?

Mungapeze Madalitso Osatha kwa Mlengi Wathu

Kodi umoyo udzakhala bwanji padziko lapansi Mulungu akadzakwanilitsa lonjezo limene anapanga kwa Abulahamu?

Kodi Munadzifunsapo?

Pezani mayankho pa mafunso onena za mavuto mu umoyo na Mulungu.