Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

NYIMBO 50

Pemphelo Yanga Yodzipelekela kwa Mulungu

Pemphelo Yanga Yodzipelekela kwa Mulungu

(Mateyu 22:37)

  1. 1. Tengani mtima wanga,

    Uzikonda co’nadi.

    Tengani mau anga,

    Aimbe motamanda.

  2. 2. Tengani manja anga;

    Agwile nchito yanu.

    Tengani cuma canga,

    Cikutumikileni.

  3. 3. Tengani moyo wanga,

    Ine nadzipeleka.

    Zocita zanga zonse

    Zikukondweletseni.

(Onaninso Sal. 40:8; Yoh. 8:29; 2 Akor. 10:5.)