Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Ganizila Moyo Wam’tsogolo

Ganizila Moyo Wam’tsogolo

Mawu a Nyimbo

  1. 1. Umoyo uyu

    Wavuta.

    Nicovuta kupilila.

    Niganizila m’tsogolo

    M’dziko ija ikubwela.

    (KOLASI)

    Ganizila nthawi ikubwela,

    Moyo udzakaladi wabwino.

    Ganizila nthawi tidzakanena,

    Zikomo M’lungu pamoyo wabwinowu.

  2. 2. Matu angawa sakumva,

    Na maso sakuonanso.

    Koma nthawi idzafika,

    Nizamvela nakuona.

    (KOLASI)

    Ganizila nthawi ikubwela,

    Moyo udzakaladi wabwino.

    Ganizila nthawi tidzakanena,

    Zikomo M’lungu pamoyo wabwinowu.

    (BILIJI)

    Siningakwanitse kuthamanga,

    Koma m’tsogolo zidzatheka.

    (KOLASI)

    Ganizila nthawi ikubwela,

    Moyo udzakaladi wabwino.

    Ganizila nthawi tidzakakondwela,

    Matsiku akhala bwino.

    (CHORUS)

    Ganizila nthawi ikubwela,

    Moyo udzakaladi wabwino.

    Ganizila nthawi tidzakanena,

    Zikomo M’lungu pamoyo wabwinowu.