Onani zimene zilipo

Kukaona Malo pa Beteli

Tikuitanani kuti mudzaone maofesi athu a nthambi, amene timayacha kuti Beteli. Maofesi ena a nthambi ali na ma miziyamu yakuti munthu akhoza kudzionela yekha zinthu popanda wina kumutsogolela.

Kuyambilanso Kukayendela Maofesi a Nthambi: Pa June 1, 2023, m'maiko ambili tinayambilanso kulola anthu kukayendela maofesi athu a nthambi. Kuti mumve zambili, funsilani ku ofesi ya nthambi imene mufuna kukayendela. Koma conde, osapitako ngati munapezeka na COVID-19, ngati muli na cimfine, kapena ngati caposacedwa munakhalako pafupi na munthu wodwala COVID-19.

Slovakia

Pekna cesta 17

831 52 BRATISLAVA 34

SLOVAK REPUBLIC

+421 2-49107611

Kuona Malo

Pa Mande mpaka pa Cisanu

8:00hrs mpaka 10:30hrs ndi 13:00hrs mpaka 15:30hrs.

Nthawi yoona malo: Ola limodzi ndi hafu

Zimene Timacita

Timayang’anila nchito ya Mboni za Yehova zoposa 26,500 za m’dzikoli ndi ku Czech Republic. Timamasulila mabuku ofotokoza Baibulo m’cinenelo ca Cisilovaki ndi cinenelo ca manja ca ku Slovakia. Timatumiza mabuku kumipingo ya m’dzikoli ndi ku Austria, Czech Republic, ndi Slovenia.

Tengani kapepala koonetsa malo.