Kodi Zopereka Zanu Zimagwiritsidwa Ntchito Bwanji?

Ntchito ya Mboni za Yehova imayendetsedwa ndi zopereka zaufulu. Werengani kuti mudziwe mmene zoperekazi zimagwiritsidwira ntchito pothandiza anthu padziko lonse.

KUFALITSA CHAKUDYA CHAUZIMU

Ntchito Yomasulira Buku Lofunika Kwambiri

Pali zinthu zambiri zomwe zimafunikira kuti Baibulo la Dziko Latsopano limasuliridwe komanso kusindikizidwa.

Mabuku a Zilembo za Anthu Osaona Akuthandiza Kwambiri

Timapanga mabuku a zilembo za anthu osaona komanso kuphunzitsa anthu kuwerenga mabukuwa.

Laibulale Yokwanira M’dzanja Limodzi

Pulogalamu ya JW Library yafotokozedwa kuti “ndi yamtengo wapatali kwambiri.” Onani zimene zimafunika kuti izikonzedwa komanso kusinthidwa.

Tchanelo cha JW Setilaiti Chimaoneka Kumene Kulibe Intaneti

Kodi abale a ku Africa amatani kuti aonere JW Broadcasting ngati alibe intaneti?

Kachipangizo Kothandiza Kwambiri

A Mboni za Yehova ambiri akutha kupanga dawunilodi mabuku ndi mavidiyo athu popanda kugwiritsa ntchito intaneti.

KUMANGA NDI KUKONZA

Maofesi a Omasulira Mabuku Omwe Akuthandiza Anthu Mamiliyoni

Dziwani mmene malo amene omasulira amagwirira ntchito yawo amakhudzira zimene akumasulira.

Ntchito Yomanga Inayenda Bwino Mliri Usanayambe

Tinakonza zoti timange kapena kukonzanso malo olambirira oposa 2,700 m’chaka cha utumiki cha 2020. Kodi mliri wa COVID-19 unakhudza bwanji zimenezi?

KUYENDETSA ZINTHU

Anateteza Ufulu wa Kulambira wa Anthu Akumidzi

Pamene anthu otsutsa anaphwanyira a Mboni za Yehova ufulu wawo wa kulambira, abale athu anawathandiza mwamsanga.

Zimene Ena Ali Nazo Zimathandizira pa Zimene Ena Akusowa

Kodi mayiko amene amapeza ndalama zochepa amathandizidwa bwanji kuti ntchito yathu iziyenda bwino?

KULALIKIRA NDI KUPHUNZITSA

Kuonera Kapena Kumvetsera Msonkhano

Msonkhano wachigawo wa chaka cha 2020 unaikidwa pa intaneti, koma anthu ambiri ku Malawi ndi ku Mozambique sangakwanitse kugwiritsa ntchito intaneti. Ndiye kodi anatha bwanji kumvetsera msonkhanowu?

Amishonale Amapita “Kumalekezero a Dziko Lapansi”

Kuli amishonale oposa 3,000 omwe akutumikira m’mayiko osiyanasiyana padziko lonse lapansi. Kodi amasamaliridwa bwanji?

Mmene Sukulu ya Giliyadi Imathandizira Padziko Lonse

Sukulu yofunika kwambiri imachitikira ku New York, koma ophunzira amachokera m’mayiko osiyanasiyana padziko lonse. Ndiye kodi ophunzirawa amayenda bwanji kuti akafike kusukuluyi?

Ntchito Yokonza Mavidiyo a Msonkhano Wachigawo wa 2020 Wakuti “Kondwerani Nthawi Zonse”

Kodi pamafunikanso zinthu ziti pokonza mavidiyo a misonkhano yathu yachigawo?

Ntchito Yomasulira Msonkhano Wachigawo wa 2020 Wakuti ‘Kondwerani Nthawi Zonse.’

Kodi n’chiyani chinathandiza kuti nkhani, masewero komanso nyimbo zimasuliridwe mofulumira kwambiri, m’zinenero zoposa 500?

Kuchita Misonkhano ya Mpingo pa Vidiyokomfelensi

Kodi gulu lathandiza bwanji mipingo kuti ikwanitse kumagwiritsa ntchito pulogalamu ya zoom yomwe ndi yotetezeka pochita misonkhano pa vidiyokomfelensi?

ZOKUGWA MWADZIDZIDZI

Kupereka Chithandizo Padziko Lonse pa Nthawi ya Mliri

Zimene tachita popereka chithandizo pa nthawi ya mliri wa COVID-19 zadabwitsa a Mboni komanso amene si Mboni.

Kuthandiza Anthu Amene Akhudzidwa Ndi Ngozi Zadzidzidzi

M’chaka chautumiki cha 2020, abale ndi alongo ambiri anakhudzidwa ndi mliri komanso ngozi zam’chilengedwe. Kodi tinawathandiza bwanji?

Mabuku a Zilembo za Anthu Osaona Akuthandiza Kwambiri

Timapanga mabuku a zilembo za anthu osaona komanso kuphunzitsa anthu kuwerenga mabukuwa.

Laibulale Yokwanira M’dzanja Limodzi

Pulogalamu ya JW Library yafotokozedwa kuti “ndi yamtengo wapatali kwambiri.” Onani zimene zimafunika kuti izikonzedwa komanso kusinthidwa.

Kuonera Kapena Kumvetsera Msonkhano

Msonkhano wachigawo wa chaka cha 2020 unaikidwa pa intaneti, koma anthu ambiri ku Malawi ndi ku Mozambique sangakwanitse kugwiritsa ntchito intaneti. Ndiye kodi anatha bwanji kumvetsera msonkhanowu?

Kupereka Chithandizo Padziko Lonse pa Nthawi ya Mliri

Zimene tachita popereka chithandizo pa nthawi ya mliri wa COVID-19 zadabwitsa a Mboni komanso amene si Mboni.

Amishonale Amapita “Kumalekezero a Dziko Lapansi”

Kuli amishonale oposa 3,000 omwe akutumikira m’mayiko osiyanasiyana padziko lonse lapansi. Kodi amasamaliridwa bwanji?

Anateteza Ufulu wa Kulambira wa Anthu Akumidzi

Pamene anthu otsutsa anaphwanyira a Mboni za Yehova ufulu wawo wa kulambira, abale athu anawathandiza mwamsanga.

Tchanelo cha JW Setilaiti Chimaoneka Kumene Kulibe Intaneti

Kodi abale a ku Africa amatani kuti aonere JW Broadcasting ngati alibe intaneti?

Maofesi a Omasulira Mabuku Omwe Akuthandiza Anthu Mamiliyoni

Dziwani mmene malo amene omasulira amagwirira ntchito yawo amakhudzira zimene akumasulira.

Kuthandiza Anthu Amene Akhudzidwa Ndi Ngozi Zadzidzidzi

M’chaka chautumiki cha 2020, abale ndi alongo ambiri anakhudzidwa ndi mliri komanso ngozi zam’chilengedwe. Kodi tinawathandiza bwanji?

Ntchito Yomasulira Buku Lofunika Kwambiri

Pali zinthu zambiri zomwe zimafunikira kuti Baibulo la Dziko Latsopano limasuliridwe komanso kusindikizidwa.

Mmene Sukulu ya Giliyadi Imathandizira Padziko Lonse

Sukulu yofunika kwambiri imachitikira ku New York, koma ophunzira amachokera m’mayiko osiyanasiyana padziko lonse. Ndiye kodi ophunzirawa amayenda bwanji kuti akafike kusukuluyi?

Ntchito Yomanga Inayenda Bwino Mliri Usanayambe

Tinakonza zoti timange kapena kukonzanso malo olambirira oposa 2,700 m’chaka cha utumiki cha 2020. Kodi mliri wa COVID-19 unakhudza bwanji zimenezi?

Zimene Ena Ali Nazo Zimathandizira pa Zimene Ena Akusowa

Kodi mayiko amene amapeza ndalama zochepa amathandizidwa bwanji kuti ntchito yathu iziyenda bwino?

Kachipangizo Kothandiza Kwambiri

A Mboni za Yehova ambiri akutha kupanga dawunilodi mabuku ndi mavidiyo athu popanda kugwiritsa ntchito intaneti.

Ntchito Yokonza Mavidiyo a Msonkhano Wachigawo wa 2020 Wakuti “Kondwerani Nthawi Zonse”

Kodi pamafunikanso zinthu ziti pokonza mavidiyo a misonkhano yathu yachigawo?

Ntchito Yomasulira Msonkhano Wachigawo wa 2020 Wakuti ‘Kondwerani Nthawi Zonse.’

Kodi n’chiyani chinathandiza kuti nkhani, masewero komanso nyimbo zimasuliridwe mofulumira kwambiri, m’zinenero zoposa 500?

Pepani, palibe mawu ofanana ndi omwe mwasankha