Mboni za Yehova Padziko Lonse

Angola

  • Luanda, Angola​—Akulalikira uthenga wa m’Baibulo m’Chipwitikizi

Mfundo Zachidule—Angola

  • 36,149,000—Chiwerengero cha anthu
  • 169,960—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 2,567—Mipingo
  • Pa anthu 221 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

KODI ZOPEREKA ZANU ZIMAGWIRITSIDWA NTCHITO BWANJI?

Kuthandiza Anthu Amene Akhudzidwa Ndi Ngozi Zadzidzidzi

M’chaka chautumiki cha 2020, abale ndi alongo ambiri anakhudzidwa ndi mliri komanso ngozi zam’chilengedwe. Kodi tinawathandiza bwanji?

NKHANI

A Mboni za Yehova Anathandiza Anthu Okhudzidwa ndi Madzi Osefukira ku Angola

Madzi atangosefukira m’chigawo cha Benguela ku Angola, a Mboni anakhazikitsa komiti yoti ithandize anthu omwe anakhudzidwa ndi ngoziyi.