Mboni za Yehova Padziko Lonse

Colombia

  • Santa Fe de Antioquia, Colombia—Akukambirana uthenga wa m’Baibulo

Mfundo Zachidule—Colombia

  • 51,673,000—Chiwerengero cha anthu
  • 186,712—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 2,271—Mipingo
  • Pa anthu 279 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

NKHANI

A Mboni Anapatsidwa Mphoto ndi Bungwe Loona Ntchito Yomasulira M’chinenero cha Manja ku Colombia

A Mboni za Yehova ku Colombia analandira mphoto ziwiri powayamikira chifukwa cha ntchito yawo yomasulira m’Chinenero Chamanja cha ku Colombia.