Pitani ku nkhani yake

FEBRUARY 19, 2020
NKHANI ZA PADZIKO LONSE

Baibulo la Dziko Latsopano Lathunthu Layamba Kupezeka M’chinenero Chamanja cha ku America

Baibulo la Dziko Latsopano Lathunthu Layamba Kupezeka M’chinenero Chamanja cha ku America

Onani zimene anthu omwe ali ndi vuto losamva ananena atalandira Baibulo la Chinenero Chamanja cha ku America ndiponso mmene lakhudzira moyo wawo.