Pitani ku nkhani yake

Kazakhstan

 

2018-06-21

KAZAKHSTAN

Anakhala M’ndende Masiku 441—Kucheza Ndi a Teymur Komanso a Mafiza Akhmedov

A Teymur Akhmedov akufotokoza zimene anakumana nazo pa nthawi imene anali m’ndende ku Kazakhstan. Iwo anakana kuchita zinthu zosemphana ndi chikumbumtima chawo ndipo anakhalabe okhulupirika kwa Yehova.

2018-05-10

KAZAKHSTAN

A Teymur Akhmedov Anakhululukidwa ndi Pulezidenti Ndipo Anatulutsidwa M’ndende

Pulezidenti wa ku Kazakhstan Nursultan Nazarbayev anakhululukira a Teymur Akhmedov omwe ndi a Mboni za Yehova, atakhala m’ndende kwa chaka ndi miyezi chifukwa chouzako ena zimene amakhulupirira. Zimenezi zachititsa kuti asakhalenso ndi mbiri yoti anapalamulapo mlandu m’dzikolo.

2015-07-20

KAZAKHSTAN

A Mboni za Yehova Anagawa Baibulo la Chinenero cha Chikazaki Pamsonkhano Komanso Pamwambo Umene Anaitanira Anthu Ambiri

A Mboni za Yehova anatulutsa Baibulo la Dziko Latsopano la Chikazaki pamsonkhano womwe unachitikira munzinda wa Almaty ku Kazakhstan.