NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA June 2022

Magazini ino ili na nkhani zophunzila kuyambila pa August 8–September 4, 2022.

NKHANI YOPHUNZILA 27

“Yembekezela Yehova”

Kodi Mudziŵa?

Kodi Aroma anali kulola munthu wopacikidwa pa mtengo, monga Yesu, kuti mtembo wake uikidwe m’manda?

Kodi Mudziŵa?

Kodi anthu ochulidwa m’Baibo anali kudziŵa bwanji poyambila caka kapena mwezi?