Mboni za Yehova Padziko Lonse

Britain

  • London, England​—⁠Akulankhula ndi anthu oyenda pansi amene akudutsa pa mlatho wa Westminster Bridge

Mfundo Zachidule—Britain

  • 66,357,000—Chiwerengero cha anthu
  • 142,073—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 1,599—Mipingo
  • Pa anthu 474 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

NTCHITO ZOMANGAMANGA

“Akazi Angathe Kugwira Nawo Ntchito ya Zomangamanga”

Mungadabwe kudziwa ntchito zimene akazi akugwira.

NTCHITO ZOMANGAMANGA

A Mboni Akuteteza Zachilengedwe Mumzinda wa Chelmsford

A Mboni za Yehova ku Britain ayamba kumanga ofesi yawo yanthambi yatsopano pafupi ndi mzinda wa Chelmsford. Kodi akuchitapo chiyani kuti ateteze zachilengedwe?