Kondwelani na Moyo Kwamuyaya!—Maphunzilo a Baibo Okambilana Komanso Zocita

Bukuli linakonzedwa kuti lizigwilitsidwa nchito pophunzila Baibo na munthu monga mbali ya pulogilamu yathu yophunzitsa Baibo kwaulele.

Pepani, palibe mawu olingana amene mwasankha.

Mungakondenso Izi

MAFUNSO AMENE AMAFUNSIDWA KAŴILI-KAŴILI

Kodi Phunzilo la Baibulo N’ciani?

Pezani mayankho a mafunso okhudza mmene timacitila phunzilo la Baibulo laulele.