Mmene Zopeleka Zanu Zimagwilila Nchito

Nchito ya Mboni za Yehova imacilikizidwa na zopeleka zaufulu. Onani mmene zopeleka zimenezi zimagwilila nchito pothandiza anthu padziko lonse.

Malo Amene Amalemekeza Mlangizi Wathu Wamkulu

Kodi malo amene amaseŵenzetsedwa cabe pa maphunzilo a zaumulungu amapindulila bwanji alangizi komanso ophunzila?

Tumasitandi twa Ulaliki Tothandiza Pocitila “Umboni ku Mitundu Yonse”

Tumasitandi twathu twa ulaliki tumazindikilidwa mosavuta pa dziko lonse. Kodi tunapangidwa bwanji?

Cikondi Capaubale Cinaonekela pa Nchito Yopeleka Thandizo mu 2022

M’caka ca 2022, kodi tinacita ciyani pothandiza anthu okhudzidwa na matsoka?

Kuwonjezela Ukhondo pa Nyumba za Ufumu Kuti Osonkhana Azikhala Otetezeka m’Nthawi ya COVID-19

Tinayambilanso kusonkhana pamasom’pamaso pa April 1, 2022. Onani zimene tinacita powonjezela ukhondo pa Nyumba za Ufumu kuti tizikhala otetezeka posonkhanamo.

Cida Cophunzitsila Baibo Cosiyana Kwambili na Zina

Buku lakuti Kondwelani na Moyo Kwamuyaya! linapangidwa na zinthu zosiyana na zimene zimagwilitsidwa nchito popanga mabuku athu ena. Ŵelengani kuti mudziŵe cifukwa cake.

Thandizo pa Matsoka a mu 2021—Abale na Alongo Athu Sananyalanyazidwe

Mu 2021, maiko ena anafunikila thandizo pa matenda a COVID-19, komanso pa matsoka ena aakulu.

Nkhani Zodalilika Komanso Zolimbitsa Cikhulupililo

Timaliyamikila kwambili danga lakuti Malo a Nkhani pa jw.org. Limatithandiza kudziŵa zimene zikucitika kwa abale na alongo athu padziko lonse. Kodi nkhanizo zimalembedwa bwanji?

Nyimbo Zimene Zimatiyandikizitsa kwa Mulungu

Kodi muli na nyimbo yopekedwa koyamba ya pamtima panu? Kodi munayamba mwaganizilapo mmene imakonzedwela?

Zidindo Zimene Zimasintha Miyoyo ya Anthu

Timapanga mabuku a anthu osaona komanso timaphunzitsa anthu kuŵelenga zilembo za anthu akhungu.

Laibulali Imene Mungathe Kuinyamula Kumanja

Anthu amakamba kuti JW Laibulali ni “yothandiza kwambili.” Ŵelengani kuti mudziŵe zimene zimafunika kuti JW Laibulali izigwila bwino nchito.

Kumvetsela Msonkhano Wacigawo pa TV na pa Wailesi

Msonkhano wacigawo wa 2020 unaikidwa pa Intaneti, koma abale na alongo ambili ku Malawi na ku Mozambique sakwanitsa kupita pa Intaneti. Kodi iwo anakwanitsa bwanji kumvetsela msonkhano wacigawo?

Kupeleka Thandizo Padziko Lonse pa Nthawi ya Mlili wa Padziko Lonse

Nchito yathu yopeleka thandizo pa nthawi ya mlili wa COVID-19 yakhala yocititsa cidwi kwa Mboni za Yehova komanso kwa anthu ena amene si Mboni.

Amishonale Akutumizidwa “Mpaka Kumalekezelo a Dziko Lapansi”

Tili na amishonale a m’munda oposa 3,000 amene akutumikila padziko lonse lapansi. Kodi iwo amasamalidwa bwanji?

Kuteteza Ufulu wa Kulambila Pakati pa Anthu Otsatila Cikhalidwe ca Makolo

Pamene anthu otsutsa anapondeleza ufulu wa Mboni za Yehova wa kulambila, abale athu anacitapo kanthu mwamsanga kuti awathandize.

Chanelo ya JW Ifika ku Madela Kumene Kulibe Intaneti

Kodi Abale athu mu Africa amaonelela bwanji mapulogilamu a JW Broadcasting ngati Intaneti kulibe?

Maofesi Omasulila Amene Amathandiza Anthu Mamiliyoni

Ŵelengani kuti mudziŵe mmene dela limene amangilako ofesi yomasulila limathandizila kuti zofalitsa zizimasulidwa momveka bwino.

Kupeleka Thandizo kwa Anthu Okhudzidwa na Matsoka

M’caka cautumiki ca 2020, abale athu mamiliyoni anakhudzidwa na mlili komanso matsoka a zacilengedwe. Kodi tinacita zotani kuti tiwathandize?

Kufalitsa Buku Lofunika Kwambili Kuposa Onse

Kumasulila, kupulinta, na kukonza Baibo ya Dziko Latsopano kumaloŵetsamo zambili mwina kuposa zimene munali kudziŵa.

Sukulu ya Giliyadi—Ophunzila Ake Amacokela Padziko Lonse

Ku New York kumacitika sukulu yofunika kwambili, koma ophunzila ake amacokela padziko lonse lapansi. Kodi ophunzila amayenda bwanji kuti akafike ku sukuluyi?

Nchito Yomanga Inayenda Bwino Mlili Usanayambe

Tinakonza zomanga na kukonzanso malo olambilila oposa 2,700 m’caka ca utumiki ca 2020. Kodi mlili wa COVID-19 unakhudza bwanji nchito imeneyi?

Zoculuka Zimathandizila pa Zimene Zikusoŵa

Kodi nchito yathu imacilikizidwa bwanji m’maiko osauka?

Kabokosi Kakang’ono Kopelekela Cakudya Cauzimu

Tsopano Mboni za Yehova zambili zingacite daunilodi zofalitsa za pa jw.org ngakhale popanda kulumikiza ku intaneti.

Kupanga Mavidiyo a Msonkhano Wacigawo wa mu 2020 Wakuti ‘Kondwelani Nthawi Zonse’!

Kodi nchito yopanga mavidiyo a misonkhano yathu yacigawo imakhala yaikulu bwanji?

Nchito Yomasulila Msonkhano Wacigawo wa 2020 Wakuti “Kondwelani Nthawi Zonse”!

Kodi zinatheka bwanji kuti nkhani, maseŵelo, na nyimbo zimasulidwe mofulumila kwambili m’zinenelo zoposa 500?

Misonkhano ya Mpingo ya pa Vidiyo Konfalensi

Kodi gulu lathandiza bwanji mipingo kugula ma akaunti a Zoom osakwela mtengo komanso otetezeka kuti izicitila misonkhano pa vidiyo konfalensi?

KUFALITSA

MAMANGIDWE NA ZOKONZA-KONZA

Kuwonjezela Ukhondo pa Nyumba za Ufumu Kuti Osonkhana Azikhala Otetezeka m’Nthawi ya COVID-19

Tinayambilanso kusonkhana pamasom’pamaso pa April 1, 2022. Onani zimene tinacita powonjezela ukhondo pa Nyumba za Ufumu kuti tizikhala otetezeka posonkhanamo.

Maofesi Omasulila Amene Amathandiza Anthu Mamiliyoni

Ŵelengani kuti mudziŵe mmene dela limene amangilako ofesi yomasulila limathandizila kuti zofalitsa zizimasulidwa momveka bwino.

Nchito Yomanga Inayenda Bwino Mlili Usanayambe

Tinakonza zomanga na kukonzanso malo olambilila oposa 2,700 m’caka ca utumiki ca 2020. Kodi mlili wa COVID-19 unakhudza bwanji nchito imeneyi?

UYANG’ANILO

Kuteteza Ufulu wa Kulambila Pakati pa Anthu Otsatila Cikhalidwe ca Makolo

Pamene anthu otsutsa anapondeleza ufulu wa Mboni za Yehova wa kulambila, abale athu anacitapo kanthu mwamsanga kuti awathandize.

Zoculuka Zimathandizila pa Zimene Zikusoŵa

Kodi nchito yathu imacilikizidwa bwanji m’maiko osauka?

KULALIKILA NA KUPHUNZITSA

Tumasitandi twa Ulaliki Tothandiza Pocitila “Umboni ku Mitundu Yonse”

Tumasitandi twathu twa ulaliki tumazindikilidwa mosavuta pa dziko lonse. Kodi tunapangidwa bwanji?

Kumvetsela Msonkhano Wacigawo pa TV na pa Wailesi

Msonkhano wacigawo wa 2020 unaikidwa pa Intaneti, koma abale na alongo ambili ku Malawi na ku Mozambique sakwanitsa kupita pa Intaneti. Kodi iwo anakwanitsa bwanji kumvetsela msonkhano wacigawo?

Amishonale Akutumizidwa “Mpaka Kumalekezelo a Dziko Lapansi”

Tili na amishonale a m’munda oposa 3,000 amene akutumikila padziko lonse lapansi. Kodi iwo amasamalidwa bwanji?

Sukulu ya Giliyadi—Ophunzila Ake Amacokela Padziko Lonse

Ku New York kumacitika sukulu yofunika kwambili, koma ophunzila ake amacokela padziko lonse lapansi. Kodi ophunzila amayenda bwanji kuti akafike ku sukuluyi?

Kupanga Mavidiyo a Msonkhano Wacigawo wa mu 2020 Wakuti ‘Kondwelani Nthawi Zonse’!

Kodi nchito yopanga mavidiyo a misonkhano yathu yacigawo imakhala yaikulu bwanji?

Nchito Yomasulila Msonkhano Wacigawo wa 2020 Wakuti “Kondwelani Nthawi Zonse”!

Kodi zinatheka bwanji kuti nkhani, maseŵelo, na nyimbo zimasulidwe mofulumila kwambili m’zinenelo zoposa 500?

Misonkhano ya Mpingo ya pa Vidiyo Konfalensi

Kodi gulu lathandiza bwanji mipingo kugula ma akaunti a Zoom osakwela mtengo komanso otetezeka kuti izicitila misonkhano pa vidiyo konfalensi?

THANDIZO PAKAGWA TSOKA

Cikondi Capaubale Cinaonekela pa Nchito Yopeleka Thandizo mu 2022

M’caka ca 2022, kodi tinacita ciyani pothandiza anthu okhudzidwa na matsoka?

Thandizo pa Matsoka a mu 2021—Abale na Alongo Athu Sananyalanyazidwe

Mu 2021, maiko ena anafunikila thandizo pa matenda a COVID-19, komanso pa matsoka ena aakulu.

Kupeleka Thandizo Padziko Lonse pa Nthawi ya Mlili wa Padziko Lonse

Nchito yathu yopeleka thandizo pa nthawi ya mlili wa COVID-19 yakhala yocititsa cidwi kwa Mboni za Yehova komanso kwa anthu ena amene si Mboni.

Kupeleka Thandizo kwa Anthu Okhudzidwa na Matsoka

M’caka cautumiki ca 2020, abale athu mamiliyoni anakhudzidwa na mlili komanso matsoka a zacilengedwe. Kodi tinacita zotani kuti tiwathandize?

Pepani, palibe mawu olingana amene mwasankha.